-
Ezekieli 40:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno ndinaona mpanda umene unazungulira kachisi.* Mʼmanja mwa munthu uja munali bango loyezera lokwana mikono 6 kutalika kwake (pa mkono uliwonse anawonjezerapo chikhatho chimodzi).* Iye anayamba kuyeza mpandawo ndipo anapeza kuti unali wochindikala bango limodzi komanso kuchoka pansi kupita mʼmwamba unali wautali bango limodzi.
-