-
Ezekieli 40:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako anayeza zipilala zamʼmbali ndipo anapeza kuti zinali zazitali mikono 60. Zinalinso chimodzimodzi ndi zipilala zamʼmbali zimene zinali mʼmageti a mbali zina za bwaloli.
-