-
Ezekieli 40:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mulifupi mwa malo owaka miyala amʼmbali mwa tinyumba tapageti munali mofanana ndi mulitali mwa tinyumbato. Malo owaka amenewa anali otsika poyerekezera ndi bwalo lamkati.
-