Ezekieli 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako munthu uja anayeza mtunda* wochokera kutsogolo kwa kanyumba kapageti lamʼmunsi kukafika pamene panayambira bwalo lamkati. Malo amenewa anali mikono 100, kumʼmawa ndi kumpoto.
19 Kenako munthu uja anayeza mtunda* wochokera kutsogolo kwa kanyumba kapageti lamʼmunsi kukafika pamene panayambira bwalo lamkati. Malo amenewa anali mikono 100, kumʼmawa ndi kumpoto.