Ezekieli 40:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Miyezo ya mawindo ake, khonde lake ndi zithunzi zake za mtengo wa kanjedza,+ inali yofanana ndi zimene zinali pakanyumba kapageti kakumʼmawa. Anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 7 ndipo khonde lake linali kutsogolo kwa masitepewo.
22 Miyezo ya mawindo ake, khonde lake ndi zithunzi zake za mtengo wa kanjedza,+ inali yofanana ndi zimene zinali pakanyumba kapageti kakumʼmawa. Anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 7 ndipo khonde lake linali kutsogolo kwa masitepewo.