-
Ezekieli 40:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kumbali iliyonse ya kanyumba kameneka komanso khonde lake kunali mawindo ofanana ndi a tinyumba tina tija. Kanyumbako kanali mikono 50 mulitali ndi mikono 25 mulifupi.
-