Ezekieli 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Khonde lake linayangʼana kubwalo lakunja ndipo pazipilala zake zamʼmbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza+ ndipo anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 8.+
31 Khonde lake linayangʼana kubwalo lakunja ndipo pazipilala zake zamʼmbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza+ ndipo anthu akafuna kulowa mʼkanyumbako amakwera masitepe 8.+