Ezekieli 40:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pafupi ndi zipilala zamʼmbali mwa tinyumba tapagetito panali chipinda chodyera komanso khomo lake, kumene ankatsukira nsembe zopsereza zathunthu.+
38 Pafupi ndi zipilala zamʼmbali mwa tinyumba tapagetito panali chipinda chodyera komanso khomo lake, kumene ankatsukira nsembe zopsereza zathunthu.+