-
Ezekieli 40:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Kumbali iliyonse ya kanyumba kapageti kunali matebulo 4 ndipo mkati mwa kanyumbako munalinso matebulo 4. Matebulo onse amene ankapherapo nyama zoti apereke nsembe analipo 8.
-