Ezekieli 40:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu uja anandiuza kuti: “Chipinda chodyeramo ichi, chimene chayangʼana kumʼmwera, ndi cha ansembe amene amagwira ntchito zokhudza utumiki wapakachisi.+
45 Munthu uja anandiuza kuti: “Chipinda chodyeramo ichi, chimene chayangʼana kumʼmwera, ndi cha ansembe amene amagwira ntchito zokhudza utumiki wapakachisi.+