Ezekieli 40:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Khondelo linali mikono 20 mulitali ndi mikono 11* mulifupi. Kuti anthu afike pakhondepo ankakwera masitepe. Pafupi ndi zipilala zamʼmbalizo panali nsanamira, imodzi mbali iyi, ina mbali inayo.+
49 Khondelo linali mikono 20 mulitali ndi mikono 11* mulifupi. Kuti anthu afike pakhondepo ankakwera masitepe. Pafupi ndi zipilala zamʼmbalizo panali nsanamira, imodzi mbali iyi, ina mbali inayo.+