Ezekieli 41:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼmbali zonse za khoma lapakhonde komanso mʼzipinda zamʼmbali za kachisi ndi pamatabwawo, munali mawindo a mafelemu aakulu mkati koma aangʼono kunja,+ ndipo anajambulamo zithunzi za mtengo wa kanjedza.
26 Mʼmbali zonse za khoma lapakhonde komanso mʼzipinda zamʼmbali za kachisi ndi pamatabwawo, munali mawindo a mafelemu aakulu mkati koma aangʼono kunja,+ ndipo anajambulamo zithunzi za mtengo wa kanjedza.