-
Ezekieli 42:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Nyumbazo zinali zosanjikizana katatu koma zinalibe zipilala ngati zamʼmabwalo. Nʼchifukwa chake zipinda zamʼmwamba zinali zazingʼono kusiyana ndi zipinda zapakati komanso zapansi.
-