-
Ezekieli 42:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mpanda wamiyala umene unali kunja, pafupi ndi zipinda zodyera unali mikono 50 mulitali mwake. Mpandawo unali mbali yakubwalo lakunja ndipo unayangʼanizana ndi zipinda zina zodyera.
-