Ezekieli 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pafupi ndi malo opanda kanthu komanso nyumba imene inali kumadzulo, mkati* mwa mpanda wamiyala wa bwalo, kumbali yakumʼmawa, kunalinso nyumba zodyera.+
10 Pafupi ndi malo opanda kanthu komanso nyumba imene inali kumadzulo, mkati* mwa mpanda wamiyala wa bwalo, kumbali yakumʼmawa, kunalinso nyumba zodyera.+