Ezekieli 42:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakati pa nyumba zodyerazo panali njira yofanana ndi ya nyumba zodyera za mbali yakumpoto.+ Mulitali ndi mulifupi mwa nyumbazo, makomo otulukira komanso kamangidwe kake zinali zofanana ndi za nyumba za kumpoto zija. Makomo ake olowera
11 Pakati pa nyumba zodyerazo panali njira yofanana ndi ya nyumba zodyera za mbali yakumpoto.+ Mulitali ndi mulifupi mwa nyumbazo, makomo otulukira komanso kamangidwe kake zinali zofanana ndi za nyumba za kumpoto zija. Makomo ake olowera