Ezekieli 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 anali ofanana ndi makomo olowera a nyumba zimene zinali kumbali yakumʼmwera zija. Pamene panayambira njira panali khomo lolowera. Khomoli linali pafupi ndi mpanda wamiyala kumbali yakumʼmawa, pamene munthu ankatha kulowera.+
12 anali ofanana ndi makomo olowera a nyumba zimene zinali kumbali yakumʼmwera zija. Pamene panayambira njira panali khomo lolowera. Khomoli linali pafupi ndi mpanda wamiyala kumbali yakumʼmawa, pamene munthu ankatha kulowera.+