Ezekieli 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe akalowa mʼnyumbazo asamatuluke mʼmalo oyerawo kupita kubwalo lakunja asanavule zovala zimene amavala potumikira,+ chifukwa zovala zimenezi nʼzopatulika. Akafuna kupita kumalo amene anthu ena onse amaloledwa kufikako, azivala zovala zina.”
14 Ansembe akalowa mʼnyumbazo asamatuluke mʼmalo oyerawo kupita kubwalo lakunja asanavule zovala zimene amavala potumikira,+ chifukwa zovala zimenezi nʼzopatulika. Akafuna kupita kumalo amene anthu ena onse amaloledwa kufikako, azivala zovala zina.”