Ezekieli 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atamaliza kuyeza malo amkati a kachisi,* ananditulutsa kunja kudzera pageti limene linayangʼana kumʼmawa+ ndipo anayeza malo onsewo.
15 Atamaliza kuyeza malo amkati a kachisi,* ananditulutsa kunja kudzera pageti limene linayangʼana kumʼmawa+ ndipo anayeza malo onsewo.