Ezekieli 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anayeza mbali yakumʼmawa ndi bango loyezera.* Mogwirizana ndi bango loyezeralo, malo onsewo anakwana mabango 500.
16 Iye anayeza mbali yakumʼmawa ndi bango loyezera.* Mogwirizana ndi bango loyezeralo, malo onsewo anakwana mabango 500.