Ezekieli 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno ndinamva wina akulankhula nane kuchokera mʼkachisi ndipo munthu uja anabwera nʼkudzaima pambali panga.+
6 Ndiyeno ndinamva wina akulankhula nane kuchokera mʼkachisi ndipo munthu uja anabwera nʼkudzaima pambali panga.+