Ezekieli 43:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano asiye kuchita zauhule ndi milungu ina ndipo achotse mitembo ya mafumu awo nʼkukaiika kutali ndi ine. Akatero ine ndidzakhala pakati pawo mpaka kalekale.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:9 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 103/1/1999, ptsa. 9, 12-13 Yesaya 2, tsa. 397
9 Tsopano asiye kuchita zauhule ndi milungu ina ndipo achotse mitembo ya mafumu awo nʼkukaiika kutali ndi ine. Akatero ine ndidzakhala pakati pawo mpaka kalekale.+