-
Ezekieli 43:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ngati atachita manyazi chifukwa cha zonse zimene anachita, uwauze za pulani ya kachisiyu, kamangidwe kake, makomo ake olowera ndi otulukira.+ Uwasonyeze pulani yake yonse komanso uwadziwitse malangizo ndi malamulo ake. Uwalembe iwo akuona nʼcholinga choti adziwe mbali zosiyanasiyana za kachisiyo nʼkumatsatira malamulo apakachisipo.+
-