-
Ezekieli 43:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Iyi ndi miyezo ya guwa lansembe pogwiritsa ntchito muyezo wa mkono+ (pa mkono uliwonse anawonjezerapo chikhatho chimodzi).* Chigawo chapansi cha guwa lansembe nʼchachitali mkono umodzi ndipo mulifupi mwake ndi mkono umodzi. Guwali lili ndi mkombero wokwana chikhatho* chimodzi mulifupi ndipo wazungulira mʼmbali mwake. Chimenechi ndi chigawo chapansi cha guwa la nsembe.
-