-
Ezekieli 43:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kuchokera pachigawo chapansi, chigawo chachiwiri cha guwa la nsembe nʼchachitali mikono iwiri ndipo mʼmbali mwake nʼchachikulu mkono umodzi kuposa chigawo chachitatu kumbali zonse. Chigawo chachitatu nʼchachitali mikono 4 ndipo mʼmbali mwake nʼchachikulu mkono umodzi kuposa malo osonkhapo moto kumbali zonse.
-