-
Ezekieli 43:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mbali zonse 4 za chigawo chachitatu ndi zokwana mikono 14 mulitali ndiponso mikono 14 mulifupi. Kakhoma kamʼmphepete mwake ndi kokwana hafu ya mkono, ndipo pansi pake ndi pokwana mkono umodzi kumbali zonse.
Masitepe a guwalo ali kumʼmawa.”
-