Ezekieli 43:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti: ‘Amenewa ndi malangizo amene akuyenera kutsatiridwa popanga guwa lansembe kuti aziperekerapo nsembe zopsereza zathunthu ndi kuwazapo magazi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:18 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, ptsa. 19-20
18 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti: ‘Amenewa ndi malangizo amene akuyenera kutsatiridwa popanga guwa lansembe kuti aziperekerapo nsembe zopsereza zathunthu ndi kuwazapo magazi.+