Ezekieli 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako utenge ngʼombe yaingʼono yamphongo ya nsembe yamachimo kuti ansembe akaipsereze pamalo apadera apakachisi, kunja kwa malo opatulika.+
21 Kenako utenge ngʼombe yaingʼono yamphongo ya nsembe yamachimo kuti ansembe akaipsereze pamalo apadera apakachisi, kunja kwa malo opatulika.+