-
Ezekieli 43:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pa tsiku lachiwiri, udzapereke mbuzi yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yamachimo. Ansembewo adzayeretse guwa lansembelo ku machimo ngati mmene analiyeretsera ku machimo popereka ngʼombe yaingʼono yamphongo.
-