-
Ezekieli 43:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ukamaliza kuyeretsa guwalo ku machimo, udzabweretse ngʼombe yaingʼono yamphongo yopanda chilema ndi nkhosa yamphongo yopanda chilema kuchokera pagulu la ziweto.
-