Ezekieli 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Udzazibweretse kwa Yehova ndipo ansembe adzaziwaze mchere+ nʼkuzipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza yathunthu.
24 Udzazibweretse kwa Yehova ndipo ansembe adzaziwaze mchere+ nʼkuzipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza yathunthu.