Ezekieli 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsiku lililonse, kwa masiku 7, uzipereka mbuzi yamphongo monga nsembe yamachimo+ komanso ngʼombe yaingʼono yamphongo ndi nkhosa yamphongo. Nyama zimenezi zizichokera pagulu la ziweto ndipo zizikhala zopanda chilema.*
25 Tsiku lililonse, kwa masiku 7, uzipereka mbuzi yamphongo monga nsembe yamachimo+ komanso ngʼombe yaingʼono yamphongo ndi nkhosa yamphongo. Nyama zimenezi zizichokera pagulu la ziweto ndipo zizikhala zopanda chilema.*