Ezekieli 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Masiku 7 amenewo akatha, kuyambira tsiku la 8+ kupita mʼtsogolo, ansembe azidzakuperekerani nsembe* zopsereza zathunthu ndi nsembe zamgwirizano paguwali, ndipo ine ndidzasangalala nanu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
27 Masiku 7 amenewo akatha, kuyambira tsiku la 8+ kupita mʼtsogolo, ansembe azidzakuperekerani nsembe* zopsereza zathunthu ndi nsembe zamgwirizano paguwali, ndipo ine ndidzasangalala nanu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”