Ezekieli 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Munthu uja anandipititsanso kugeti lakunja la malo opatulika, limene linayangʼana kumʼmawa+ ndipo tinapeza kuti linali lotseka.+
44 Munthu uja anandipititsanso kugeti lakunja la malo opatulika, limene linayangʼana kumʼmawa+ ndipo tinapeza kuti linali lotseka.+