-
Ezekieli 44:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mukabweretsa alendo amene ndi osachita mdulidwe wamumtima ndi mdulidwe wa khungu lawo nʼkulowa nawo mʼmalo anga opatulika, iwo amadetsa kachisi wanga. Mumapereka mkate wanga, mafuta ndi magazi, pamene mukuphwanya pangano langa chifukwa cha zonyansa zanu zonse zimene mukuchita.
-