Ezekieli 44:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu simunasamalire zinthu zanga zopatulika.+ Mʼmalomwake munasankha anthu ena kuti azigwira ntchito zapamalo anga opatulika mʼmalo mwa inu.”
8 Inu simunasamalire zinthu zanga zopatulika.+ Mʼmalomwake munasankha anthu ena kuti azigwira ntchito zapamalo anga opatulika mʼmalo mwa inu.”