-
Ezekieli 44:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 ‘Sadzayandikira kwa ine kuti anditumikire monga ansembe kapena kuyandikira zinthu zanga zilizonse zoyera kapena zoyera koposa. Iwo adzachita manyazi chifukwa cha zinthu zonyansa zimene anachita.
-