Ezekieli 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo akalowa mʼtinyumba tamʼmageti a bwalo lamkati, azivala zovala zansalu.+ Akamatumikira mʼtinyumba tamʼmageti a bwalo lamkati kapena mkati mwenimwenimo, asamavale chovala chilichonse cha ubweya wa nkhosa.
17 Iwo akalowa mʼtinyumba tamʼmageti a bwalo lamkati, azivala zovala zansalu.+ Akamatumikira mʼtinyumba tamʼmageti a bwalo lamkati kapena mkati mwenimwenimo, asamavale chovala chilichonse cha ubweya wa nkhosa.