Ezekieli 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo azivala nduwira zansalu kumutu kwawo ndi makabudula ansalu aatali.+ Asamavale chovala chilichonse chimene chingachititse kuti atuluke thukuta.
18 Iwo azivala nduwira zansalu kumutu kwawo ndi makabudula ansalu aatali.+ Asamavale chovala chilichonse chimene chingachititse kuti atuluke thukuta.