Ezekieli 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Asanapite kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira+ nʼkuziika mʼzipinda zodyera zopatulika.*+ Akatero azivala zovala zina kuti asachititse kuti anthu akhale oyera chifukwa cha zovala zawozo.
19 Asanapite kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira+ nʼkuziika mʼzipinda zodyera zopatulika.*+ Akatero azivala zovala zina kuti asachititse kuti anthu akhale oyera chifukwa cha zovala zawozo.