Ezekieli 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo asamakwatire mkazi wamasiye kapena amene mwamuna wake anamusiya ukwati.+ Koma angathe kukwatira namwali yemwe ndi mbadwa ya Isiraeli kapena mkazi wamasiye amene anali mkazi wa wansembe.+
22 Iwo asamakwatire mkazi wamasiye kapena amene mwamuna wake anamusiya ukwati.+ Koma angathe kukwatira namwali yemwe ndi mbadwa ya Isiraeli kapena mkazi wamasiye amene anali mkazi wa wansembe.+