Ezekieli 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati pali mlandu, iwo ndi amene akuyenera kukhala oweruza+ ndipo aziweruza motsatira malamulo anga.+ Azisunga malamulo ndi malangizo anga okhudza zikondwerero zanga+ zonse ndipo aziyeretsa masabata anga.
24 Ngati pali mlandu, iwo ndi amene akuyenera kukhala oweruza+ ndipo aziweruza motsatira malamulo anga.+ Azisunga malamulo ndi malangizo anga okhudza zikondwerero zanga+ zonse ndipo aziyeretsa masabata anga.