Ezekieli 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo asamayandikire munthu aliyense wakufa kuopera kuti angakhale odetsedwa. Koma wansembe akhoza kudzidetsa chifukwa cha bambo ake, mayi ake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi, mchimwene wake kapena mchemwali wake amene ndi wosakwatiwa.+
25 Iwo asamayandikire munthu aliyense wakufa kuopera kuti angakhale odetsedwa. Koma wansembe akhoza kudzidetsa chifukwa cha bambo ake, mayi ake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi, mchimwene wake kapena mchemwali wake amene ndi wosakwatiwa.+