Ezekieli 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limene adzalowe mʼmalo oyera, mʼbwalo lamkati, kuti akatumikire mʼmalo oyerawo, adzapereke nsembe yake yamachimo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
27 Pa tsiku limene adzalowe mʼmalo oyera, mʼbwalo lamkati, kuti akatumikire mʼmalo oyerawo, adzapereke nsembe yake yamachimo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.