Ezekieli 45:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita chikondwerero cha Pasika.+ Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda zofufumitsa.+
21 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita chikondwerero cha Pasika.+ Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda zofufumitsa.+