Ezekieli 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Kanyumba kapageti la bwalo lamkati kamene kayangʼana kumʼmawa+ kazikhala kotseka+ kwa masiku 6 ogwira ntchito.+ Koma pa tsiku la Sabata ndi pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka kazitsegulidwa.
46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Kanyumba kapageti la bwalo lamkati kamene kayangʼana kumʼmawa+ kazikhala kotseka+ kwa masiku 6 ogwira ntchito.+ Koma pa tsiku la Sabata ndi pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka kazitsegulidwa.