Ezekieli 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amʼdzikoli azigwadanso nʼkuwerama pamaso pa Yehova pakhomo lolowera mʼkanyumba kameneka pa masiku a Sabata ndi pa masiku amene mwezi watsopano waoneka.+
3 Anthu amʼdzikoli azigwadanso nʼkuwerama pamaso pa Yehova pakhomo lolowera mʼkanyumba kameneka pa masiku a Sabata ndi pa masiku amene mwezi watsopano waoneka.+