Ezekieli 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nsembe yopsereza yathunthu imene mtsogoleri wa anthu azipereka kwa Yehova pa tsiku la Sabata, izikhala ana a nkhosa amphongo 6 ndi nkhosa yamphongo imodzi. Nyama zonsezi zizikhala zopanda chilema.+
4 Nsembe yopsereza yathunthu imene mtsogoleri wa anthu azipereka kwa Yehova pa tsiku la Sabata, izikhala ana a nkhosa amphongo 6 ndi nkhosa yamphongo imodzi. Nyama zonsezi zizikhala zopanda chilema.+