Ezekieli 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka, azipereka ngʼombe yaingʼono yamphongo yopanda chilema kuchokera pagulu la ziweto. Aziperekanso ana a nkhosa amphongo 6 ndi nkhosa imodzi yamphongo. Nyama zonsezi zizikhala zopanda chilema.+
6 Pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka, azipereka ngʼombe yaingʼono yamphongo yopanda chilema kuchokera pagulu la ziweto. Aziperekanso ana a nkhosa amphongo 6 ndi nkhosa imodzi yamphongo. Nyama zonsezi zizikhala zopanda chilema.+