Ezekieli 46:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtsogoleri wa anthu akamalowa, azidzera mbali yakukhonde ya kanyumba kapageti ndipo akamatuluka azidzeranso komweko.+
8 Mtsogoleri wa anthu akamalowa, azidzera mbali yakukhonde ya kanyumba kapageti ndipo akamatuluka azidzeranso komweko.+